msonkhano wa gulu lanu losunga usanayambe · 2020. 9. 3. · mtunda wa mamita awiri pakati panu...

3
MAMITA AWIRI Pelekani moni kwa ena pogwiritsa ntchito bayibayi wa dzanja MSONKHANO WA GULU LANU LOSUNGA USANAYAMBE Phimbani mphuno komanso pa kamwa panu (KHALANI KUNYUMBA NGATI MUKUMVA KUTI MUKUDWALA) Sambani mmanja kapena gwiritsani sanitayiza kwa mphindi imodzi

Upload: others

Post on 30-Mar-2021

1 views

Category:

Documents


0 download

TRANSCRIPT

Page 1: MSONKHANO WA GULU LANU LOSUNGA USANAYAMBE · 2020. 9. 3. · mtunda wa mamita awiri pakati panu WIRI Ikani bokosi la ndalama pakatikati pa gulu MSONKHANO WAGULU LANU LOSUNGA UKUCHITIKA

MAMITA AWIRI

Pelekani moni kwa ena pogwiritsa ntchito bayibayi

wa dzanja

MSONKHANO WA GULU LANU LOSUNGA

USANAYAMBE

Phimbani mphuno komanso pa kamwa panu

(KHALANI KUNYUMBA NGATI MUKUMVA KUTI MUKUDWALA)

Sambani mmanja kapena gwiritsani sanitayiza kwa

mphindi imodzi

Page 2: MSONKHANO WA GULU LANU LOSUNGA USANAYAMBE · 2020. 9. 3. · mtunda wa mamita awiri pakati panu WIRI Ikani bokosi la ndalama pakatikati pa gulu MSONKHANO WAGULU LANU LOSUNGA UKUCHITIKA

Khalani motalikilana mtunda wa mamita awiri pakati panuMAMITA AWIRI

Ikani bokosi la ndalama pakatikati pa gulu

MSONKHANO WAGULU LANU LOSUNGA

UKUCHITIKA

Sambani m’manja musanagwire ndalama

komanso mutatha kugwira ndalama

MAMITA AWIRI

Page 3: MSONKHANO WA GULU LANU LOSUNGA USANAYAMBE · 2020. 9. 3. · mtunda wa mamita awiri pakati panu WIRI Ikani bokosi la ndalama pakatikati pa gulu MSONKHANO WAGULU LANU LOSUNGA UKUCHITIKA

Mudzipita m’modzi panthawi kukayika ndalama mubokosi

(M’NYUMBA KAPENA PABWALO)

MSONKHANO WAGULU LANU LOSUNGA

UKUCHITIKA