imbani fonimwaulere 54747 - unicef 19 poster in... · covid 19 posters 2020 chichewa.cdr author:...

4
Tsekani pakamwa ndi mphuno potsokomola kapena kuyetsemula ndi kansalu, kapena popinda mkono wanu ndi kutsokomolera kapena kuyetsemulira m'kati mwa mkonowo pamene mwaupindapo. Matenda a Coronavirus ndiwopeweka Produced by Health Education Services of the Ministry of Health Imbani foni mwaulere 54747 World Health Organization

Upload: others

Post on 06-Nov-2020

1 views

Category:

Documents


0 download

TRANSCRIPT

Page 1: Imbani fonimwaulere 54747 - UNICEF 19 Poster in... · Covid 19 POSTERS 2020 chichewa.cdr Author: Rodgers Chilemba Created Date: 3/23/2020 9:39:55 AM

Tsekani pakamwa ndi mphuno potsokomola kapena kuyetsemula ndi kansalu, kapena popinda mkono wanu ndi kutsokomolera

kapena kuyetsemulira m'kati mwa mkonowo pamene mwaupindapo.

Matenda a Coronavirus ndiwopeweka

Produced by Health Education Services of the Ministry of Health

Imbani foni

mwaulere

54747

World HealthOrganization

Page 2: Imbani fonimwaulere 54747 - UNICEF 19 Poster in... · Covid 19 POSTERS 2020 chichewa.cdr Author: Rodgers Chilemba Created Date: 3/23/2020 9:39:55 AM

Sambani m’manja ndi Sopo moyenera nthawi zonse

kuti mupewe matenda a Coronavirus.

Matenda a Coronavirus ndiwopeweka

Produced by Health Education Services of the Ministry of Health

Imbani foni

mwaulere

54747

World HealthOrganization

Page 3: Imbani fonimwaulere 54747 - UNICEF 19 Poster in... · Covid 19 POSTERS 2020 chichewa.cdr Author: Rodgers Chilemba Created Date: 3/23/2020 9:39:55 AM

Anyamata ndi asungwana sambani m’manja ndi Sopo nthawi

zonse kuti mupewe matenda a Coronavirus.

Matenda a Coronavirus ndiwopeweka

Produced by Health Education Services of the Ministry of Health

Imbani foni

mwaulere

54747

World HealthOrganization

Page 4: Imbani fonimwaulere 54747 - UNICEF 19 Poster in... · Covid 19 POSTERS 2020 chichewa.cdr Author: Rodgers Chilemba Created Date: 3/23/2020 9:39:55 AM

Makolo titengepo gawo posambitsa ana m’manja ndi sopo nthawi zonse kuti tipewe matenda a Coronavirus

Matenda a Coronavirus ndiwopeweka

Produced by Health Education Services of the Ministry of Health

Imbani foni

mwaulere

54747

World HealthOrganization